Home / Languages / Chichewa

Chichewa

Sunnah of Musaafahah – Chichewa

Asilamu awiri atakumana. Patatha miyedzi iwiri kapena itatu mu lock down. Zoona zake ndi chisangalaro komanso chikodwelero ndiye nkhani ndiyakuti kugwirana manja wina ndi mnzake monga mmene machitidwe amtumiki wathu ( Sallalahu alayhi wa sallam) sunnah. Monga omutsatira masahaba Radhiyallahu anhum amkachitira. Nthawi iti! Nthawi pamene, Munthu wina ndi mnzake …

Read More »